Ephraim Mkali Banda amene akuziwika ndidzina loti The True Son of Malawi, akhala pa mpepo (on air)
Pakalipano akugwira ntchoto ndi Adventist Word Radio ku Tanzania, Akugwira ntchito ngati mu ulutsi, IT personel komanso ngati oyang'aira mapologalamu a chizungu, ena mwamapologalamu amene amapanga ndiawa, Sunset, Lifestyle ndi Acappella
Ana badwa uchaka cha 1983 ku nkhata bay, ndimwana woyamba kwa bambo ndi mai Michal Banda.
No comments:
Post a Comment